Suffix | Cholinga Lyrics

2,174 Views

VERSE 1

African Gospel award//baptism yanga ku tchalitchi
mukandimva Ndikupha Sound apolisi osandimanga eh ndimaimbira Jesus
Fellowship ndi ma Tradi//Care for girls and Fight Cancer Initiative
Mukandimva ndili pa air kundiona pa TV ndili Pa Stage ulendo ngwa kwa Jesus (wazizuR)

Bridge

Munjira tikumana ndi mikondo//Kutumikila chauta ndi nkhondo
Osamatopa kupinda Maondo// follow follow me as I follow ze Leader Londo

Hook

WaniBEKA MBWE nkhuTemwa a neba umo nkhujitemwera ine (Cholinga Changa Nkaone Yesu)
WaniBEKA ni kuNjanja Njanja MaTurn up pa stage abale (Cholinga Changa Nkaone Yesu)
Ah Cholinga Changa (Cholinga Changa) Cholinga Changa (Cholinga Changa) Cholinga Changa imwe (Cholinga Changa nkaone Yesu)

VERSE 2

Dziko ndi loopsya koma Ambuye akutiSAMALA//Tchimo ndi loopsya ona Ambuye akuti SAMALA
Obedience ndiphunzitseni//Popanda Inuyo INeyo Inuyo singazakuoneni
Munandimenyera Ufulu//Za Ukapolozi Ine Totoizi Ngati Fulu
Ndine mFulu ku dziko Ndine mfulu ku Tchimo//Ndimadabula ufulu izi zokha ndiye si Tchimo

Bridge
Munjira tikumana ndi mikondo//Kutumikila chauta ndi nkhondo
Osamatopa kupinda Maondo//follow follow me as I follow ze leader londo

HOOK
WaniBEKA MBWE nkhuTemwa a neba umo nkhujitemwera ine (Cholinga Changa Nkaone Yesu)
WaniBEKA ni kuNjanja Njanja MaTurn up pa stage abale (Cholinga Changa Nkaone Yesu)
Ah Cholinga Changa (Cholinga Changa) Cholinga Changa (Cholinga Changa) Cholinga Changa imwe (Cholinga Changa nkaone Yesu)

Bridge

Kid (Cholinga Changa nkaone Yesu X2)
Kids (Munjira tikumana ndi mikondo//Kutumikila chauta ndi nkhondo